Agalatiya 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma mwana amene anabadwa kwa kapolo wamkazi uja anabadwa monga mmene ana onse amabadwira,+ pamene mwana winayo amene anabadwa kwa mkazi yemwe anali mfulu anabadwa kudzera mu lonjezo.+
23 Koma mwana amene anabadwa kwa kapolo wamkazi uja anabadwa monga mmene ana onse amabadwira,+ pamene mwana winayo amene anabadwa kwa mkazi yemwe anali mfulu anabadwa kudzera mu lonjezo.+