Agalatiya 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ngakhale zili choncho, kodi Malemba amati chiyani? “Thamangitsani kapolo wamkaziyu pamodzi ndi mwana wakeyu pano, chifukwa mwana wa kapolo ameneyu sadzakhala wolandira cholowa pamodzi ndi mwana wa mkazi amene ndi mfulu.”+ Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:30 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, tsa. 21
30 Ngakhale zili choncho, kodi Malemba amati chiyani? “Thamangitsani kapolo wamkaziyu pamodzi ndi mwana wakeyu pano, chifukwa mwana wa kapolo ameneyu sadzakhala wolandira cholowa pamodzi ndi mwana wa mkazi amene ndi mfulu.”+