Agalatiya 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu amene mukufuna kuti muzionedwa kuti ndinu olungama chifukwa chotsatira chilamulo,+ mwadzilekanitsa ndi Khristu. Ndipo mwachititsa kuti musadzalandirenso kukoma mtima kwake kwakukulu.
4 Inu amene mukufuna kuti muzionedwa kuti ndinu olungama chifukwa chotsatira chilamulo,+ mwadzilekanitsa ndi Khristu. Ndipo mwachititsa kuti musadzalandirenso kukoma mtima kwake kwakukulu.