-
Agalatiya 5:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Koma kudzera mwa mzimu, ife tikuyembekezera mwachidwi zimene zidzatichitikire chifukwa choonedwa kuti ndife olungama, chifukwa cha chikhulupiriro.
-