Agalatiya 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Abale, munaitanidwa kuti mukhale aufulu. Koma musagwiritse ntchito ufulu umenewu ngati mwayi woti muzichita zimene thupi lomwe si langwiro limalakalaka.+ Mʼmalomwake muzilola kuti chikondi chizikulimbikitsani kutumikirana.+ Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:13 Nsanja ya Olonda,5/15/2010, tsa. 272/15/2010, tsa. 113/15/1992, tsa. 20
13 Abale, munaitanidwa kuti mukhale aufulu. Koma musagwiritse ntchito ufulu umenewu ngati mwayi woti muzichita zimene thupi lomwe si langwiro limalakalaka.+ Mʼmalomwake muzilola kuti chikondi chizikulimbikitsani kutumikirana.+