Agalatiya 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa zimene thupi limalakalaka zimalimbana ndi mzimu ndipo mzimu nawonso umalimbana ndi thupi. Zinthu ziwiri zimenezi zimatsutsana kuti musachite zinthu zimene mumafuna kuchita.+
17 Chifukwa zimene thupi limalakalaka zimalimbana ndi mzimu ndipo mzimu nawonso umalimbana ndi thupi. Zinthu ziwiri zimenezi zimatsutsana kuti musachite zinthu zimene mumafuna kuchita.+