Agalatiya 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ngati tikutsogoleredwa ndi mzimu pa moyo wathu, tiyeni tipitirize kuchita zinthu mogwirizana ndi mzimuwo.+
25 Ngati tikutsogoleredwa ndi mzimu pa moyo wathu, tiyeni tipitirize kuchita zinthu mogwirizana ndi mzimuwo.+