Aefeso 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musatchule ngakhale nkhani zokhudza khalidwe lochititsa manyazi, nkhani zopusa kapena nthabwala zotukwana+ chifukwa ndi zinthu zosayenera. Mʼmalomwake muziyamika Mulungu.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:4 Galamukani!,6/8/2003, tsa. 13
4 Musatchule ngakhale nkhani zokhudza khalidwe lochititsa manyazi, nkhani zopusa kapena nthabwala zotukwana+ chifukwa ndi zinthu zosayenera. Mʼmalomwake muziyamika Mulungu.+