-
Afilipi 1:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Inde, kuti ndikadzabweranso kwa inu chisangalalo chanu chidzasefukire chifukwa ndinu otsatira a Khristu Yesu.