Akolose 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikufuna kuti mudziwe mavuto aakulu amene ndikukumana nawo chifukwa cha inuyo ndi anthu a ku Laodikaya+ komanso chifukwa cha anthu onse amene sanandionepo maso ndi maso.* Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:1 Nsanja ya Olonda,7/15/2009, ptsa. 3-4
2 Ndikufuna kuti mudziwe mavuto aakulu amene ndikukumana nawo chifukwa cha inuyo ndi anthu a ku Laodikaya+ komanso chifukwa cha anthu onse amene sanandionepo maso ndi maso.*