Akolose 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngakhale kuti sindili kumeneko, ndikuganizirabe za inu. Ndasangalala kumva kuti mumachita zinthu mwadongosolo+ komanso kuti muli ndi chikhulupiriro cholimba mwa Khristu.+
5 Ngakhale kuti sindili kumeneko, ndikuganizirabe za inu. Ndasangalala kumva kuti mumachita zinthu mwadongosolo+ komanso kuti muli ndi chikhulupiriro cholimba mwa Khristu.+