Akolose 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Popeza muli naye pa ubwenzi munadulidwa ndipo mdulidwe wake sunali wochitidwa ndi manja a anthu koma unachitika pamene munavula thupi lauchimo,+ chifukwa mdulidwe wa atumiki a Khristu umakhala wotero.+
11 Popeza muli naye pa ubwenzi munadulidwa ndipo mdulidwe wake sunali wochitidwa ndi manja a anthu koma unachitika pamene munavula thupi lauchimo,+ chifukwa mdulidwe wa atumiki a Khristu umakhala wotero.+