1 Atesalonika 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nʼchifukwa chake abale, mʼmavuto athu onse* komanso mʼmasautso athu onse tatonthozedwa chifukwa cha inu komanso chifukwa cha kukhulupirika kumene mukusonyeza.+
7 Nʼchifukwa chake abale, mʼmavuto athu onse* komanso mʼmasautso athu onse tatonthozedwa chifukwa cha inu komanso chifukwa cha kukhulupirika kumene mukusonyeza.+