1 Timoteyo 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu onse amene ndi akapolo aziona kuti ambuye awo ndi oyenera kuwalemekeza ndi mtima wonse,+ kuti dzina la Mulungu ndiponso zimene amatiphunzitsa zisanyozedwe.+ 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:1 Nsanja ya Olonda,2/1/1991, tsa. 21
6 Anthu onse amene ndi akapolo aziona kuti ambuye awo ndi oyenera kuwalemekeza ndi mtima wonse,+ kuti dzina la Mulungu ndiponso zimene amatiphunzitsa zisanyozedwe.+