-
1 Timoteyo 6:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Komanso akapolo amene ambuye awo ndi Akhristu, asamawachitire zinthu mopanda ulemu poona kuti ndi abale. Mʼmalomwake, azigwira ntchito mwakhama kwambiri, chifukwa ntchito yawo yabwinoyo ikuthandiza Akhristu anzawo omwe amawakonda.
Pitiriza kuphunzitsa zinthu zimenezi ndiponso kulimbikitsa anthu kuti azichita zimenezi.
-