1 Timoteyo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngati munthu akuphunzitsa zinthu zabodza, ndipo sakuvomereza malangizo abwino+ ochokera kwa Ambuye wathu Yesu Khristu, ndiponso zinthu zimene timaphunzira zogwirizana ndi kudzipereka kwathu kwa Mulungu,+
3 Ngati munthu akuphunzitsa zinthu zabodza, ndipo sakuvomereza malangizo abwino+ ochokera kwa Ambuye wathu Yesu Khristu, ndiponso zinthu zimene timaphunzira zogwirizana ndi kudzipereka kwathu kwa Mulungu,+