1 Timoteyo 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 munthu ameneyo ndi wodzitukumula ndiponso wonyada ndipo samvetsa kalikonse.+ Mʼmalomwake, amakonda kukangana ndiponso kutsutsana pa mawu.+ Zimenezi zimayambitsa nsanje, mikangano, kunenerana mawu achipongwe* ndiponso kuganizirana zoipa.
4 munthu ameneyo ndi wodzitukumula ndiponso wonyada ndipo samvetsa kalikonse.+ Mʼmalomwake, amakonda kukangana ndiponso kutsutsana pa mawu.+ Zimenezi zimayambitsa nsanje, mikangano, kunenerana mawu achipongwe* ndiponso kuganizirana zoipa.