1 Timoteyo 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zimachititsanso kuti anthu opotoka maganizo+ ndiponso osadziwa choonadi, azikangana pa zinthu zazingʼono poganiza kuti kukhala wodzipereka kwa Mulungu ndi njira yopezera phindu.+ 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:5 Nsanja ya Olonda,7/15/2002, tsa. 128/15/1988, tsa. 5
5 Zimachititsanso kuti anthu opotoka maganizo+ ndiponso osadziwa choonadi, azikangana pa zinthu zazingʼono poganiza kuti kukhala wodzipereka kwa Mulungu ndi njira yopezera phindu.+