-
2 Timoteyo 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mofanana ndi Yane ndi Yambure, amene anatsutsa Mose, anthu amenewanso akupitiriza kutsutsa choonadi. Iwo ali ndi maganizo opotoka kwambiri, ndipo sakuyenerera chikhulupirirochi.
-