2 Timoteyo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ukudziwanso mmene ndinazunzikira komanso masautso amene ndinakumana nawo ku Antiokeya,+ ku Ikoniyo+ ndi ku Lusitara.+ Komabe ndinapirira ndipo Ambuye anandipulumutsa ku zonsezi.+ 2 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:11 Nsanja ya Olonda,2/15/2013, ptsa. 28-29
11 Ukudziwanso mmene ndinazunzikira komanso masautso amene ndinakumana nawo ku Antiokeya,+ ku Ikoniyo+ ndi ku Lusitara.+ Komabe ndinapirira ndipo Ambuye anandipulumutsa ku zonsezi.+