-
Tito 1:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Mmodzi wa iwo, amenenso ndi mneneri wawo, ananena kuti: “Akerete ndi anthu abodza nthawi zonse, zilombo zolusa zakutchire ndiponso alesi osusuka.”
-