-
Aheberi 2:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Munamutsitsa pangʼono poyerekeza ndi angelo. Munamuveka ulemerero ndi ulemu ngati chisoti chachifumu ndipo munamuika kuti azilamulira ntchito za manja anu.
-