Aheberi 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwaika zinthu zonse pansi pa mapazi ake.”+ Popeza Mulungu anaika zinthu zonse pansi pa Mwana wake,+ ndiye kuti palibe chilichonse chimene anasiya osachiika pansi pa Mwanayo.+ Komabe, panopa sitikuona kuti zinthu zonse zili pansi pake.+
8 Mwaika zinthu zonse pansi pa mapazi ake.”+ Popeza Mulungu anaika zinthu zonse pansi pa Mwana wake,+ ndiye kuti palibe chilichonse chimene anasiya osachiika pansi pa Mwanayo.+ Komabe, panopa sitikuona kuti zinthu zonse zili pansi pake.+