Aheberi 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso pamene akunena kuti: “Ine ndidzamudalira.”+ Ndiponso kuti: “Taonani! Ine ndi ana amene Yehova* wandipatsa.”+
13 Komanso pamene akunena kuti: “Ine ndidzamudalira.”+ Ndiponso kuti: “Taonani! Ine ndi ana amene Yehova* wandipatsa.”+