Aheberi 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho iye anayenera kukhala ngati “abale” ake pa zinthu zonse,+ kuti akhale mkulu wa ansembe wachifundo komanso wokhulupirika pa zinthu zokhudza Mulungu, nʼcholinga choti apereke nsembe yophimba machimo a anthu+ kuti tigwirizanenso ndi Mulungu. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:17 Nsanja ya Olonda,4/15/2007, tsa. 212/1/2007, ptsa. 20-21
17 Choncho iye anayenera kukhala ngati “abale” ake pa zinthu zonse,+ kuti akhale mkulu wa ansembe wachifundo komanso wokhulupirika pa zinthu zokhudza Mulungu, nʼcholinga choti apereke nsembe yophimba machimo a anthu+ kuti tigwirizanenso ndi Mulungu.