Aheberi 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yesu akuyenera kupatsidwa ulemerero waukulu+ kuposa Mose, chifukwa womanga nyumba amakhala wolemekezeka kuposa nyumbayo. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:3 Nsanja ya Olonda,7/15/1998, tsa. 11
3 Yesu akuyenera kupatsidwa ulemerero waukulu+ kuposa Mose, chifukwa womanga nyumba amakhala wolemekezeka kuposa nyumbayo.