Aheberi 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa timachita nawo zimene Khristu akuchita, ngati zinthu zimene tinkadalira poyamba tazigwira mwamphamvu mpaka mapeto.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:14 Nsanja ya Olonda,5/1/1996, ptsa. 21-24
14 Chifukwa timachita nawo zimene Khristu akuchita, ngati zinthu zimene tinkadalira poyamba tazigwira mwamphamvu mpaka mapeto.+