-
Aheberi 3:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Nanga kodi analumbirira ndani kuti sadzalowa mumpumulo wake? Kodi si omwe aja amene sanamumvere?