-
Aheberi 6:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Nthaka imalandira madalitso kuchokera kwa Mulungu ikamwa madzi a mvula imene imagwera panthakapo kawirikawiri. Kenako imatulutsa zomera zimene zimathandiza amene ailima.
-