-
Aheberi 6:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Koma ngakhale kuti tikulankhula chonchi, sitikukayikira kuti pa nkhani ya zinthu zobweretsa chipulumutso, inu okondedwa muli pabwino kusiyana ndi amene anagwa aja.
-