Aheberi 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamene Mulungu analonjeza Abulahamu, analumbira pa dzina lake chifukwa panalibe wina wamkulu kuposa iyeyo amene akanamulumbirira.+
13 Pamene Mulungu analonjeza Abulahamu, analumbira pa dzina lake chifukwa panalibe wina wamkulu kuposa iyeyo amene akanamulumbirira.+