Aheberi 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa anthu polumbira amatchula winawake wamkulu kuposa iwowo, ndipo lumbiro lawo limathetsa mkangano uliwonse chifukwa lumbirolo limatsimikizira mwalamulo zomwe munthu wanena.+
16 Chifukwa anthu polumbira amatchula winawake wamkulu kuposa iwowo, ndipo lumbiro lawo limathetsa mkangano uliwonse chifukwa lumbirolo limatsimikizira mwalamulo zomwe munthu wanena.+