Aheberi 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mofanana ndi zimenezi, Mulungu anafuna kutsimikizira anthu olandira lonjezolo+ kuti chifuniro chake sichingasinthe. Choncho anachita kulumbira pa zimene analonjezazo.
17 Mofanana ndi zimenezi, Mulungu anafuna kutsimikizira anthu olandira lonjezolo+ kuti chifuniro chake sichingasinthe. Choncho anachita kulumbira pa zimene analonjezazo.