Aheberi 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Popeza analibe bambo, analibe mayi, analibe mzere wa makolo ndipo tsiku limene anabadwa komanso limene anamwalira silikudziwika, koma anamuchititsa kuti afanane ndi Mwana wa Mulungu, iye ndi wansembe mpaka kalekale.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:3 Nsanja ya Olonda,11/15/1995, tsa. 1911/15/1993, tsa. 312/1/1989, tsa. 17
3 Popeza analibe bambo, analibe mayi, analibe mzere wa makolo ndipo tsiku limene anabadwa komanso limene anamwalira silikudziwika, koma anamuchititsa kuti afanane ndi Mwana wa Mulungu, iye ndi wansembe mpaka kalekale.+