Aheberi 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho mungaone kuti munthuyu anali wofunika kwambiri. Moti kholo lathu Abulahamu, anamupatsa chakhumi pa zinthu zabwino kwambiri zimene anatenga kunkhondo.+
4 Choncho mungaone kuti munthuyu anali wofunika kwambiri. Moti kholo lathu Abulahamu, anamupatsa chakhumi pa zinthu zabwino kwambiri zimene anatenga kunkhondo.+