Aheberi 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zoonadi mogwirizana ndi Chilamulo, ana aamuna a Levi+ amene amapatsidwa udindo wa unsembe, analamulidwa kuti azilandira zakhumi kuchokera kwa anthu.+ Anthu amenewa anali abale awo ngakhale kuti abale awowo anali mbadwa za Abulahamu.
5 Zoonadi mogwirizana ndi Chilamulo, ana aamuna a Levi+ amene amapatsidwa udindo wa unsembe, analamulidwa kuti azilandira zakhumi kuchokera kwa anthu.+ Anthu amenewa anali abale awo ngakhale kuti abale awowo anali mbadwa za Abulahamu.