Aheberi 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma munthu ameneyu, yemwe sanachokere mumzere wobadwira wa Levi analandira chakhumi kuchokera kwa Abulahamu, ndipo anadalitsa Abulahamuyo amene analandira malonjezo kuchokera kwa Mulungu.+
6 Koma munthu ameneyu, yemwe sanachokere mumzere wobadwira wa Levi analandira chakhumi kuchokera kwa Abulahamu, ndipo anadalitsa Abulahamuyo amene analandira malonjezo kuchokera kwa Mulungu.+