Aheberi 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Alevi ankalandira zakhumi ndipo ndi anthu oti amafa. Koma munthu wina amene analandira zakhumi, Malemba amamuchitira umboni kuti ali moyo.+
8 Alevi ankalandira zakhumi ndipo ndi anthu oti amafa. Koma munthu wina amene analandira zakhumi, Malemba amamuchitira umboni kuti ali moyo.+