Aheberi 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu amene akufotokozedwa pamenepa ndi wa fuko lina ndipo palibe aliyense wa fuko limenelo amene anatumikirapo paguwa lansembe.+
13 Munthu amene akufotokozedwa pamenepa ndi wa fuko lina ndipo palibe aliyense wa fuko limenelo amene anatumikirapo paguwa lansembe.+