Aheberi 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mkulu wa ansembe ngati ameneyu ndi wotiyeneradi chifukwa ndi wokhulupirika, wosalakwa, wosaipitsidwa,+ wosiyana ndi anthu ochimwa ndipo wakwezedwa pamwamba kwambiri.+
26 Mkulu wa ansembe ngati ameneyu ndi wotiyeneradi chifukwa ndi wokhulupirika, wosalakwa, wosaipitsidwa,+ wosiyana ndi anthu ochimwa ndipo wakwezedwa pamwamba kwambiri.+