Aheberi 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa zimene tikunenazi, mfundo yaikulu ndi yakuti: Tili ndi mkulu wa ansembe ngati ameneyu,+ ndipo iye wakhala kudzanja lamanja la mpando wachifumu wa Wolemekezeka kumwamba.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:1 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 161 Sukulu ya Utumiki, ptsa. 29-31
8 Pa zimene tikunenazi, mfundo yaikulu ndi yakuti: Tili ndi mkulu wa ansembe ngati ameneyu,+ ndipo iye wakhala kudzanja lamanja la mpando wachifumu wa Wolemekezeka kumwamba.+