Aheberi 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mkulu wa ansembe aliyense amaikidwa kuti azipereka mphatso ndiponso nsembe. Choncho uyunso anafunika kukhala ndi chinachake choti apereke.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:3 Nsanja ya Olonda,8/15/2000, tsa. 14
3 Mkulu wa ansembe aliyense amaikidwa kuti azipereka mphatso ndiponso nsembe. Choncho uyunso anafunika kukhala ndi chinachake choti apereke.+