Aheberi 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zinthu zimenezi zitakonzedwa chonchi, nthawi ndi nthawi ansembe ankalowa mʼchipinda choyamba kukachita mautumiki opatulika.+
6 Zinthu zimenezi zitakonzedwa chonchi, nthawi ndi nthawi ansembe ankalowa mʼchipinda choyamba kukachita mautumiki opatulika.+