Aheberi 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chihema chimenecho chinali chifaniziro cha nthawi inoyo+ ndipo mogwirizana ndi chifanizirocho, mphatso ndiponso nsembe zimaperekedwa.+ Komabe, zimenezi sizipangitsa munthu amene akuchita utumiki wopatulikayo kukhala ndi chikumbumtima choyera.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:9 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2023, ptsa. 25-26
9 Chihema chimenecho chinali chifaniziro cha nthawi inoyo+ ndipo mogwirizana ndi chifanizirocho, mphatso ndiponso nsembe zimaperekedwa.+ Komabe, zimenezi sizipangitsa munthu amene akuchita utumiki wopatulikayo kukhala ndi chikumbumtima choyera.+