Aheberi 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Popeza Chilamulo chimangochitira chithunzi+ zinthu zabwino zimene zikubwera+ ndipo si zinthu zenizenizo, sichingachititse* amene amalambira Mulungu kukhala angwiro pogwiritsa ntchito nsembe zimene amapereka mosalekeza chaka chilichonse.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:1 Nsanja ya Olonda,8/15/2000, tsa. 17
10 Popeza Chilamulo chimangochitira chithunzi+ zinthu zabwino zimene zikubwera+ ndipo si zinthu zenizenizo, sichingachititse* amene amalambira Mulungu kukhala angwiro pogwiritsa ntchito nsembe zimene amapereka mosalekeza chaka chilichonse.+