Aheberi 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa cha chikhulupiriro, Abulahamu+ ataitanidwa, anamvera nʼkupita kumalo amene ankayembekezera kuwalandira ngati cholowa. Iye anapitadi, ngakhale kuti sankadziwa kumene akupita.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:8 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2020, ptsa. 3-4
8 Chifukwa cha chikhulupiriro, Abulahamu+ ataitanidwa, anamvera nʼkupita kumalo amene ankayembekezera kuwalandira ngati cholowa. Iye anapitadi, ngakhale kuti sankadziwa kumene akupita.+