Aheberi 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Bambo athu otibereka ankatilanga ndipo tinkawalemekeza. Ndiye kuli bwanji Atate wa moyo wathu wauzimu? Kodi sitiyenera kuwagonjera koposa pamenepo kuti tikhale ndi moyo?+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:9 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),9/2019, ptsa. 14-15
9 Bambo athu otibereka ankatilanga ndipo tinkawalemekeza. Ndiye kuli bwanji Atate wa moyo wathu wauzimu? Kodi sitiyenera kuwagonjera koposa pamenepo kuti tikhale ndi moyo?+