Aheberi 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kulinso Yesu, mkhalapakati+ wa pangano latsopano,+ ndiponso magazi amene awazidwa, omwe amalankhula mʼnjira yabwino kwambiri kuposa magazi a Abele.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:24 Nsanja ya Olonda,12/15/2008, ptsa. 13-14
24 Kulinso Yesu, mkhalapakati+ wa pangano latsopano,+ ndiponso magazi amene awazidwa, omwe amalankhula mʼnjira yabwino kwambiri kuposa magazi a Abele.+