-
Aheberi 12:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Mawu akuti “ndidzagwedezanso,” akusonyeza kuti zinthu zimene adzazigwedezezo zidzachotsedwa ndipo zinthu zimenezi sizinapangidwe ndi Mulungu. Adzazichotsa kuti zomwe sizikugwedezeka zitsale.
-