-
Aheberi 12:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Choncho, popeza kuti tidzalandira Ufumu umene sungagwedezeke, tiyeni tikhalebe okhulupirika kuti Mulungu apitirize kutisonyeza kukoma mtima kwakukulu, kuti tizichita utumiki wopatulika mʼnjira yovomerezeka, moopa Mulungu komanso mwaulemu kwambiri.
-